Luka 20:19 BL92

19 Ndipo alembi ndi ansembe akuru anafunafuna kumgwira ndi manja nthawi yomweyo; ndipo anaopa anthu; pakuti anazindikira kuti ananenera pa iwo fanizo ili.

Werengani mutu wathunthu Luka 20

Onani Luka 20:19 nkhani