24 Tandionetsani Ine rupiya latheka. Cithunzithunzi ndi colemba cace nca yani? Anati iwo, Ca Kaisara.
Werengani mutu wathunthu Luka 20
Onani Luka 20:24 nkhani