Luka 20:29 BL92

29 Tsono panali abale asanu ndi awiri; ndipo woyamba anakwatira mkazi, nafa wopanda mwana;

Werengani mutu wathunthu Luka 20

Onani Luka 20:29 nkhani