Luka 21:14 BL92

14 Cifukwa cace tsimikizani mumtima mwanu, kuti usanafike mlandu musalingirire cimene mudzayankha.

Werengani mutu wathunthu Luka 21

Onani Luka 21:14 nkhani