37 Ndipo usana uli wonse iye analikuphunzitsa m'Kacisi; ndi usiku uli wonse anaturuka, nagona pa phiri lochedwa la Azitona.
Werengani mutu wathunthu Luka 21
Onani Luka 21:37 nkhani