Luka 21:4 BL92

4 pakuti onse amenewa anaika mwa unyinji wao pa zoperekazo; koma iye mwa kusowa kwace anaikamo za moyo wace, zonse anali nazo.

Werengani mutu wathunthu Luka 21

Onani Luka 21:4 nkhani