7 Ndipo iwo anamfunsa iye, nati, Mphunzitsi, nanga zinthu izi zidzaoneka liti? ndipo cizindikilo ndi cianipamene izi ziti zicitike?
Werengani mutu wathunthu Luka 21
Onani Luka 21:7 nkhani