Luka 21:9 BL92

9 Ndipo pamene mudzamva za nkhondo ndi mapanduko, musaopsedwa; pakuti ziyenera izi ziyambe kucitika; koma mathedwe sakhala pomwepo.

Werengani mutu wathunthu Luka 21

Onani Luka 21:9 nkhani