Luka 22:42 BL92

42 nati, Atate, mukafuna Inu, cotsani cikho ici pa Ine; koma si kufuna kwanga ai, komatu kwanu kucitike.

Werengani mutu wathunthu Luka 22

Onani Luka 22:42 nkhani