Luka 22:54 BL92

54 Ndipo 7 pamenepo anamgwira iye, napita naye, nalowa m'nyumba ya mkulu wa ansembe. Koma Petro anatsata kutari.

Werengani mutu wathunthu Luka 22

Onani Luka 22:54 nkhani