Luka 23:7 BL92

7 Ndipo m'mene anadziwa kuti ali wa m'ulamuliro wace wa Herode, anamtumiza iye kwa Herode, amene anali iye mwini ku Yerusalemu masiku awa,

Werengani mutu wathunthu Luka 23

Onani Luka 23:7 nkhani