Luka 24:12 BL92

12 Koma Petro ananyamuka nathamangira kumanda, ndipo powerama anaona nsaru zoyera pa zokha; ndipo anacoka nanka kwao, nazizwa ndi cija cidacitikaco.

Werengani mutu wathunthu Luka 24

Onani Luka 24:12 nkhani