Luka 24:21 BL92

21 Ndipo tinayembekeza ife kuti iye ndiye wakudzayo kudzaombola Israyeli, Komatunso, pamodzi ndi izi zonse lero ndilo tsiku lacitatu kuyambira zidacitika izi.

Werengani mutu wathunthu Luka 24

Onani Luka 24:21 nkhani