Luka 24:39 BL92

39 Penyani manja anga ndi mapazianga, kuti Ine ndine mwini: 2 ndikhudzeni, ndipo penyani; pakuti mzimu ulibe, mnofu ndi mafupa, monga muona ndirinazo Ine.

Werengani mutu wathunthu Luka 24

Onani Luka 24:39 nkhani