Luka 4:34 BL92

34 Ha! tiri ndi ciani ndi Inu, Yesu wa ku N azarete? kodi munadza kutiononga ife? ndikudziwani Inu muli yani, ndinu Woyera wace wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Luka 4

Onani Luka 4:34 nkhani