Luka 4:43 BL92

43 Koma anati kwa iwo, Kundiyenera Ine ndilalikire Uthenga Wabwino wa Ufumu wa Mulungu ku midzi yinanso: cifukwa ndinatumidwa kudzatero.

Werengani mutu wathunthu Luka 4

Onani Luka 4:43 nkhani