Luka 5:20 BL92

20 Ndipo iye, pakuona cikhulupiriro cao, anati, Munthu iwe, macimo ako akhululukidwa.

Werengani mutu wathunthu Luka 5

Onani Luka 5:20 nkhani