Luka 5:25 BL92

25 Ndipo pomwepo anaimirira pamaso pao, nasenza cimene adagonapo, nacokapo, kunka kunyumba kwace, wakulemekeza Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Luka 5

Onani Luka 5:25 nkhani