Luka 5:27 BL92

27 Ndipo zitatha izi iye anaturuka, Danna munthu wamsonkho, dzina lace Levi, alikukhala polandira msonkho, nati kwa iye, Unditsate Ine.

Werengani mutu wathunthu Luka 5

Onani Luka 5:27 nkhani