Luka 5:35 BL92

35 Koma masiku adzafika; ndipo pamene mkwati adzacotsedwa kwa iwo, pamenepo adzasala kudya masiku omwewo.

Werengani mutu wathunthu Luka 5

Onani Luka 5:35 nkhani