Luka 5:39 BL92

39 Ndipo palibe munthu atamwa vinyo wakale afuna watsopano; pakuti anena, Wakale ali wokoma.

Werengani mutu wathunthu Luka 5

Onani Luka 5:39 nkhani