Luka 6:12 BL92

12 Ndipo kunali masiku awa, iye anaturuka nanka kuphiri kukapemphera; nacezera usiku wonse m'kupemphera kwa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Luka 6

Onani Luka 6:12 nkhani