22 Odala inu, pamene anthu adzada inu, nadzapatula inu, nadzatonza inu, nadzalitaya dzina lanu monga loipa, cifukwa ca Mwana wa munthu.
Werengani mutu wathunthu Luka 6
Onani Luka 6:22 nkhani