Luka 6:25 BL92

25 Tsoka inu okhuta tsopano! cifukwa mudzamva njala, Tsoka inu, akuseka tsopano! cifukwa mudzacita maliro ndi kulira misozi.

Werengani mutu wathunthu Luka 6

Onani Luka 6:25 nkhani