Luka 6:29 BL92

29 Iye amene akupanda iwe pa tsaya limodzi umpatsenso linzace; ndi iye amene alanda copfunda cako, usamkanize malaya ako.

Werengani mutu wathunthu Luka 6

Onani Luka 6:29 nkhani