36 Khalani inu acifundo monga Atate wanu ali wacifundo. Ndipo musamaweruza, ndipo simudzaweruzidwa.
Werengani mutu wathunthu Luka 6
Onani Luka 6:36 nkhani