Luka 7:11 BL92

11 Ndipo kunali, katapita kamphindi, iye ana pita kumudzi, dzina lace Nayini; ndipo ophunzira ace ndi mpingo waukuru wa anthu anapita nave.

Werengani mutu wathunthu Luka 7

Onani Luka 7:11 nkhani