Luka 7:16 BL92

16 Ndipo mantha anagwira onsewo: ndipo analemekeza Mulungu, nanena kuti, Mneneri wamkuru wauka mwa ife; ndipo Mulungu wadzaceza ndi anthu ace.

Werengani mutu wathunthu Luka 7

Onani Luka 7:16 nkhani