Luka 7:19 BL92

19 Ndipo Yohane anaitana awiri a ophunzira ace, nawatuma kwa Ambuye, nanena, Kodi ndinu wakudzayo, kapena tiyang'anire wina?

Werengani mutu wathunthu Luka 7

Onani Luka 7:19 nkhani