Luka 7:25 BL92

25 Koma munaturuka kukaona ciani? Munthu wobvala zobvala zofewa kodi? Onani, iwo akubvala zolemera, ndi akukhala odyerera, ali m'makuka a mafumu.

Werengani mutu wathunthu Luka 7

Onani Luka 7:25 nkhani