Luka 7:28 BL92

28 Ndinena kwa inu, kuti, Mwa akubadwa ndi akazi palibe mmodzi wamkuru woposa Yohane; koma iye amene ali wamng'ono mu Ufumu wa Mulungu amposa iye.

Werengani mutu wathunthu Luka 7

Onani Luka 7:28 nkhani