Luka 7:34 BL92

34 Mwana wa munthu wafika wakudya ndi wakumwa; ndipo munena, Onani, munthu wosusuka ndi wakumwaimwa vinyo, bwenzi la amisonkho ndi anthu ocimwa!

Werengani mutu wathunthu Luka 7

Onani Luka 7:34 nkhani