Luka 8:21 BL92

21 Koma iye anayankha, nati kwa iwo, Amai wanga ndi abale anga ndiwo amene akumva mau a Mulungu, nawacita.

Werengani mutu wathunthu Luka 8

Onani Luka 8:21 nkhani