Luka 8:33 BL92

33 Ndipo ziwandazo zinaturuka mwa munthu nizilowa mu nkhumba: ndipo gululo linatsika liwiro potsetsereka ndi kulowa m'nyanjamo, nilitsamwa.

Werengani mutu wathunthu Luka 8

Onani Luka 8:33 nkhani