Luka 8:41 BL92

41 Ndipo onani, panadza munthu dzina lace Yairo, ndipo iye ndiye mkuru wa sunagoge; ndipo anagwa pamapazi ace a Yesu, nampempha iye adze kunyumba kwace;

Werengani mutu wathunthu Luka 8

Onani Luka 8:41 nkhani