11 Koma unyinji wa anthu, pamene anadziwa, anamtsata Iye; ndipo iye anawalandira, nalankhula nao za Ufumu wa Mulungu, naciritsa amene anasowa kuciritsidwa.
Werengani mutu wathunthu Luka 9
Onani Luka 9:11 nkhani