Luka 9:18 BL92

18 Ndipo kunali, pamene iye analikupemphera padera, ophunzira anali naye; ndipo anawafunsa iwo, kuti, Makamuwo a anthu anena kuti Ine ndine yani?

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:18 nkhani