Luka 9:24 BL92

24 Pakutiamene ali yense akafuna kupulumutsa moyo wace, iye adzautaya; koma amene ali yense akataya moyo wace cifukwa ca Ine, iye adzaupulumutsa uwu.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:24 nkhani