Luka 9:32 BL92

32 Koma Petro ndi iwo anali naye analemedwa ndi tulo; koma m'mene anayera m'maso ndithu, anaona ulemerero wace, ndi amuna awiriwo akuimirira ndi iye.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:32 nkhani