Luka 9:43 BL92

43 Ndipo onse anadabwa pa ukulu wace wa Mulungu.Koma pamene onse analikuzizwa ndi zonse anazicita, iye anati kwa ophunzira ace,

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:43 nkhani