Luka 9:49 BL92

49 Ndipo Yohane anayankha nati, Ambuye, tinaona wina alikuturutsa ziwanda m'dzina lanu; ndipo tinamletsa, cifukwa satsatana nafe.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:49 nkhani