Luka 9:53 BL92

53 Ndipo iwo sanamlandira iye, cifukwa nkhope yace inali yoloza kunka ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:53 nkhani