Luka 9:60 BL92

60 Koma anati kwa iye, Leka akufa aike akufa a eni okha; koma muka iwe nubukitse mbiri yace ya Ufumu wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:60 nkhani