Luka 9:9 BL92

9 Ndipo Herode anati, Yohane ndinamdula mutu ine; koma uyu ndani ndikumva zotere za iye? Ndipo anafunafuna kumuona iye.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:9 nkhani