20 Pomwepo Iye anayamba kutonza midziyo, m'mene zinacitidwa zambiri za nchito zamphamvu zace, cifukwa kuti siinatembenuke.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 11
Onani Mateyu 11:20 nkhani