Mateyu 22:24 BL92

24 nanena, Mphunzitsi, Mose anati, Ngati munthu akafa wopanda mwana, mphwace adzakwatira mkazi wace, nadzamuukitsira mbale wace mbeu.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 22

Onani Mateyu 22:24 nkhani