Mateyu 22:25 BL92

25 Tsono panali ndi ife abale asanu ndi awiri; ndipo wakuyamba anakwatira, namwalira wopanda mbeu, nasiyira mphwace mkazi wace;

Werengani mutu wathunthu Mateyu 22

Onani Mateyu 22:25 nkhani