1 Samueli 1:1 BL92

1 NDIPO panali munthu wina wa ku Ramatayimu Zofimu, wa dziko la mapiri la Efraimu, dzina lace ndiye Elikana, mwana wace wa Yerohamu, mwana wa Elihu, mwana wa Tohu, mwana wa Zufu, M-efraimu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1

Onani 1 Samueli 1:1 nkhani