1 Samueli 1:13 BL92

13 Koma Hana ananena mu mtima; milomo yace inatukula, koma mau ace sanamveka; cifukwa cace Eli anamuyesa woledzera.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1

Onani 1 Samueli 1:13 nkhani