15 Ndipo Hana anayankha, nati, Iai, mbuyanga. Ine ndiri mkazi wa mtima wacisoni; sindinamwa vinyo kapena cakumwa cowawa, koma ndinatsanulira mtima wanga pamaso pa Yehova.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1
Onani 1 Samueli 1:15 nkhani